Numeri 7:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Komanso anapereka ng’ombe yaing’ono yamphongo imodzi, nkhosa imodzi yamphongo, ndi mwana wa nkhosa mmodzi wamphongo wosapitirira chaka chimodzi. Nyama zimenezi zinali za nsembe yopsereza.+
69 Komanso anapereka ng’ombe yaing’ono yamphongo imodzi, nkhosa imodzi yamphongo, ndi mwana wa nkhosa mmodzi wamphongo wosapitirira chaka chimodzi. Nyama zimenezi zinali za nsembe yopsereza.+