Numeri 7:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Anaperekanso chikho chimodzi chagolide cholemera masekeli 10, chodzaza ndi zofukiza.+