Numeri 7:84 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Potsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri+ a Isiraeli anapereka izi: Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva+ 12, zikho zagolide 12.
84 Potsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri+ a Isiraeli anapereka izi: Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva+ 12, zikho zagolide 12.