Numeri 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo Aroni anayamba kuchitadi zimenezo. Anayatsa nyalezo kuti ziwalitse malo apatsogolo pa choikapo nyalecho,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.
3 Ndipo Aroni anayamba kuchitadi zimenezo. Anayatsa nyalezo kuti ziwalitse malo apatsogolo pa choikapo nyalecho,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.