Numeri 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno upereke Aleviwo pamaso pa Yehova, ndipo ana a Isiraeliwo aike+ manja awo pa Aleviwo.+