Numeri 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndi operekedwa. Aperekedwa kwa ine kuchokera pakati pa ana a Isiraeli.+ Ine ndikuwatenga iwowa m’malo mwa onse otsegula mimba ya mayi awo, oyamba kubadwa onse pakati pa ana a Isiraeli.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:16 Nsanja ya Olonda,4/15/1992, tsa. 12
16 Amenewa ndi operekedwa. Aperekedwa kwa ine kuchokera pakati pa ana a Isiraeli.+ Ine ndikuwatenga iwowa m’malo mwa onse otsegula mimba ya mayi awo, oyamba kubadwa onse pakati pa ana a Isiraeli.+