Numeri 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho m’malo mwa ana oyamba kubadwa onse a Isiraeli, ndikutenga Alevi kuti akhale anga.+