-
Numeri 8:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Mose ndi Aroni ndi khamu lonse la ana a Isiraeli, anachita zonse zofunikira kwa Alevi. Ana a Isiraeliwo anachitira Aleviwo malinga ndi zonse zimene Yehova analamula Mose zokhudza Alevi.
-