Numeri 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’mwezi woyamba*+ wa chaka chachiwiri, ana a Isiraeli atatuluka m’dziko la Iguputo, Yehova analankhula ndi Mose m’chipululu cha Sinai. Iye anati:
9 M’mwezi woyamba*+ wa chaka chachiwiri, ana a Isiraeli atatuluka m’dziko la Iguputo, Yehova analankhula ndi Mose m’chipululu cha Sinai. Iye anati: