Numeri 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Mose anawayankha kuti: “Dikirani pomwepo, ndimve zimene Yehova ati alamule zokhudza inu.”+
8 Pamenepo Mose anawayankha kuti: “Dikirani pomwepo, ndimve zimene Yehova ati alamule zokhudza inu.”+