Numeri 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu wina aliyense mwa inu kapena mwa mbadwa zanu, amene wadetsedwa pokhudza mtembo wa munthu,+ kapena amene ali pa ulendo wautali, akonzebe nsembe ya pasika yopereka kwa Yehova. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:10 Nsanja ya Olonda,2/1/1993, tsa. 31
10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu wina aliyense mwa inu kapena mwa mbadwa zanu, amene wadetsedwa pokhudza mtembo wa munthu,+ kapena amene ali pa ulendo wautali, akonzebe nsembe ya pasika yopereka kwa Yehova.