Numeri 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku lomanga chihema chopatulika,+ mtambo unaima pamwamba pa chihema cha Umbonicho.+ Koma kuyambira madzulo mpaka m’mawa, moto+ unali kuoneka pamwamba pa chihema chopatulikacho.
15 Pa tsiku lomanga chihema chopatulika,+ mtambo unaima pamwamba pa chihema cha Umbonicho.+ Koma kuyambira madzulo mpaka m’mawa, moto+ unali kuoneka pamwamba pa chihema chopatulikacho.