Numeri 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Yehova akalamula, ana a Isiraeli anali kunyamuka, ndipo Yehova akalamula, anali kumanga msasa.+ Masiku onse amene mtambo unali pamwamba pa chihemacho, iwo anali kukhalabe pamsasapo.
18 Choncho Yehova akalamula, ana a Isiraeli anali kunyamuka, ndipo Yehova akalamula, anali kumanga msasa.+ Masiku onse amene mtambo unali pamwamba pa chihemacho, iwo anali kukhalabe pamsasapo.