Numeri 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi zina mtambowo unali kungokhala masiku owerengeka pamwamba pa chihemapo. Yehova akalamula,+ iwo anali kukhalabe pamsasapo, ndipo Yehova akalamula, iwo anali kuchoka.
20 Nthawi zina mtambowo unali kungokhala masiku owerengeka pamwamba pa chihemapo. Yehova akalamula,+ iwo anali kukhalabe pamsasapo, ndipo Yehova akalamula, iwo anali kuchoka.