Numeri 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nthawi zina mtambowo+ unali kukhalapo kuchokera madzulo kufika m’mawa, ndipo m’mawawo mtambowo unali kuchoka, anthuwo n’kunyamuka. Kaya mtambowo uchoke masana kapena usiku, iwonso anali kunyamuka.+
21 Nthawi zina mtambowo+ unali kukhalapo kuchokera madzulo kufika m’mawa, ndipo m’mawawo mtambowo unali kuchoka, anthuwo n’kunyamuka. Kaya mtambowo uchoke masana kapena usiku, iwonso anali kunyamuka.+