Numeri 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kaya mtambowo ukhale pamwamba pa chihemacho masiku awiri, mwezi, kapena masiku ambiri, ana a Isiraeli anali kukhalabe pamsasa osachoka. Koma mtambowo ukanyamuka, iwo anali kuchoka.+
22 Kaya mtambowo ukhale pamwamba pa chihemacho masiku awiri, mwezi, kapena masiku ambiri, ana a Isiraeli anali kukhalabe pamsasa osachoka. Koma mtambowo ukanyamuka, iwo anali kuchoka.+