Numeri 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akaliza malipenga onse awiriwo, khamu lonse lizisunga pangano la msonkhano ndi iwe, ndipo lizifika pakhomo la chihema chokumanako.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2020, ptsa. 30-31
3 Akaliza malipenga onse awiriwo, khamu lonse lizisunga pangano la msonkhano ndi iwe, ndipo lizifika pakhomo la chihema chokumanako.+