Numeri 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Aroni, ansembewo, ndiwo aziliza malipengawo.+ Ndi lamulo kwa inu kugwiritsa ntchito malipengawa m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.*
8 Ana a Aroni, ansembewo, ndiwo aziliza malipengawo.+ Ndi lamulo kwa inu kugwiritsa ntchito malipengawa m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.*