Numeri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anasamuka malinga ndi malangizo amene Yehova anapereka kudzera kwa Mose.+ Kameneka kanali koyamba kuti iwo asamuke.
13 Iwo anasamuka malinga ndi malangizo amene Yehova anapereka kudzera kwa Mose.+ Kameneka kanali koyamba kuti iwo asamuke.