Numeri 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Zebuloni anali Eliyabu, mwana wa Heloni.+