Numeri 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Akohati, onyamula zinthu za m’malo opatulika+ ananyamuka, kuti pokafika akapeze chihema chopatulika chitamangidwa kale.
21 Kenako Akohati, onyamula zinthu za m’malo opatulika+ ananyamuka, kuti pokafika akapeze chihema chopatulika chitamangidwa kale.