Numeri 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Efuraimu+ ananyamuka m’magulu awo. Mtsogoleri wa asilikali awo anali Elisama,+ mwana wa Amihudi.
22 Ndiyeno a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Efuraimu+ ananyamuka m’magulu awo. Mtsogoleri wa asilikali awo anali Elisama,+ mwana wa Amihudi.