Numeri 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Manase+ anali Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.