Numeri 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pomaliza, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Dani+ ananyamuka. Iwo ndiwo anali olonda kumbuyo kwa zigawo zonse za mafukowo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.
25 Pomaliza, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Dani+ ananyamuka. Iwo ndiwo anali olonda kumbuyo kwa zigawo zonse za mafukowo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.