Numeri 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Nafitali+ anali Ahira,+ mwana wa Enani.