Numeri 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma pamene anthuwo anayamba kulirira Mose, iye anapembedzera Yehova+ ndipo motowo unazima.