Numeri 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 koma mudzaidya kwa mwezi wonse wathunthu, mpaka idzatulukira m’mphuno mwanu, ndipo mudzachita kunyansidwa nayo.+ Zidzatero chifukwa mwakana Yehova amene ali pakati panu, ndipo mukum’lirira kuti: “Tinachokeranji ku Iguputo?”’”+
20 koma mudzaidya kwa mwezi wonse wathunthu, mpaka idzatulukira m’mphuno mwanu, ndipo mudzachita kunyansidwa nayo.+ Zidzatero chifukwa mwakana Yehova amene ali pakati panu, ndipo mukum’lirira kuti: “Tinachokeranji ku Iguputo?”’”+