Numeri 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo Mose anapita kukauza anthuwo mawu a Yehova. Anasonkhanitsa amuna 70 kuchokera pa akulu a anthuwo, n’kuwauza kuti aimirire mozungulira chihema chokumanako.+
24 Pamenepo Mose anapita kukauza anthuwo mawu a Yehova. Anasonkhanitsa amuna 70 kuchokera pa akulu a anthuwo, n’kuwauza kuti aimirire mozungulira chihema chokumanako.+