Numeri 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma sindikutero ndi mtumiki wanga Mose.+ Iye ndamuikiza nyumba yanga yonse.+