Numeri 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:10 Nsanja ya Olonda,8/1/2004, tsa. 26
10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+