Numeri 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kodi bambo ake akanam’lavulira+ malovu kumaso, sakanakhala wonyazitsidwa masiku 7? Choncho m’tulutseni+ akakhale kunja kwa msasa masiku 7,+ pambuyo pake mum’landire mumsasamo.”+
14 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kodi bambo ake akanam’lavulira+ malovu kumaso, sakanakhala wonyazitsidwa masiku 7? Choncho m’tulutseni+ akakhale kunja kwa msasa masiku 7,+ pambuyo pake mum’landire mumsasamo.”+