Numeri 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambuyo pake, anthuwo anachoka ku Hazeroti,+ n’kukamanga msasa m’chipululu cha Parana.+