Numeri 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana onse a Isiraeli anayamba kudandaula za Mose ndi Aroni.+ Ndipo khamu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera m’chipululu muno. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:2 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 15
2 Ana onse a Isiraeli anayamba kudandaula za Mose ndi Aroni.+ Ndipo khamu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera m’chipululu muno.