Numeri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+
10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+