Numeri 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso, pali ine Mulungu wamoyo, dziko lonse lapansi lidzadzaza ndi ulemerero wa Yehova.+