Numeri 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘“Komanso, ana anu amene munati adzatengedwa ndi adani,+ nawonso ndidzawalowetsa m’dzikolo ndithu. Moti dziko limene inuyo mwalikana, iwo adzalidziwa bwino.+
31 “‘“Komanso, ana anu amene munati adzatengedwa ndi adani,+ nawonso ndidzawalowetsa m’dzikolo ndithu. Moti dziko limene inuyo mwalikana, iwo adzalidziwa bwino.+