Numeri 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ana anu adzakhala abusa m’chipululu+ kwa zaka 40, ndipo adzavutika chifukwa cha kusakhulupirika*+ kwanu, mpaka womalizira kufa wa inu atagona m’manda m’chipululu.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:33 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, ptsa. 30-31
33 Ana anu adzakhala abusa m’chipululu+ kwa zaka 40, ndipo adzavutika chifukwa cha kusakhulupirika*+ kwanu, mpaka womalizira kufa wa inu atagona m’manda m’chipululu.+