Numeri 14:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Komanso amuna amene Mose anawatuma kukazonda dzikolo, amene atabwerako anapangitsa anthu onse kudandaula motsutsana ndi Mose, mwa kunena zoipa zokhudza dzikolo,+
36 Komanso amuna amene Mose anawatuma kukazonda dzikolo, amene atabwerako anapangitsa anthu onse kudandaula motsutsana ndi Mose, mwa kunena zoipa zokhudza dzikolo,+