Numeri 14:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kumeneko mukakumana ndi Aamaleki ndi Akanani,+ ndithu akakuphani ndi lupanga. Chifukwa mwasiya kutsatira Yehova, Yehovayo sapita nanu kumeneko.”+
43 Kumeneko mukakumana ndi Aamaleki ndi Akanani,+ ndithu akakuphani ndi lupanga. Chifukwa mwasiya kutsatira Yehova, Yehovayo sapita nanu kumeneko.”+