Numeri 14:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Komabe, anthuwo ananyamuka mwa iwo okha ulendo wopita kudera lamapiri kuja,+ koma likasa la pangano la Yehova silinachoke pakati pa msasa. Mose nayenso sanachoke.+
44 Komabe, anthuwo ananyamuka mwa iwo okha ulendo wopita kudera lamapiri kuja,+ koma likasa la pangano la Yehova silinachoke pakati pa msasa. Mose nayenso sanachoke.+