Numeri 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 woperekayo azikapereka ng’ombe yamphongoyo limodzi ndi nsembe yambewu.+ Nsembe yambewuyo izikakhala yokwanira magawo atatu a magawo 10 a ufa wosalala a muyezo wa efa. Ufawo azikauthira mafuta okwanira hafu ya muyezo wa hini.
9 woperekayo azikapereka ng’ombe yamphongoyo limodzi ndi nsembe yambewu.+ Nsembe yambewuyo izikakhala yokwanira magawo atatu a magawo 10 a ufa wosalala a muyezo wa efa. Ufawo azikauthira mafuta okwanira hafu ya muyezo wa hini.