Numeri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu amene mwapanga mpingo limodzi ndi alendo amene akukhala pakati panu, mukhale ndi malamulo amodzi.+ Amenewa ndiwo malamulo amene inuyo muziwatsatira mpaka kalekale m’mibadwo yanu. Mlendo azikhala chimodzimodzi ndi inu pamaso pa Yehova.+
15 Inu amene mwapanga mpingo limodzi ndi alendo amene akukhala pakati panu, mukhale ndi malamulo amodzi.+ Amenewa ndiwo malamulo amene inuyo muziwatsatira mpaka kalekale m’mibadwo yanu. Mlendo azikhala chimodzimodzi ndi inu pamaso pa Yehova.+