Numeri 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Munthu ameneyo wanyoza mawu a Yehova,+ ndipo waphwanya malamulo ake.+ Aziphedwa ndithu mosalephera.+ Mlandu wa cholakwa chake uzikhala ndi iye mwini.’”+
31 Munthu ameneyo wanyoza mawu a Yehova,+ ndipo waphwanya malamulo ake.+ Aziphedwa ndithu mosalephera.+ Mlandu wa cholakwa chake uzikhala ndi iye mwini.’”+