Numeri 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi ndi chinthu chaching’ono kuti Mulungu anakuyandikizani kwa iye, limodzi ndi abale anu onse, ana a Levi? Kodi tsopano anthu inu mukufunanso udindo waunsembe?+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:10 Nsanja ya Olonda,8/1/2000, ptsa. 10-11
10 Kodi ndi chinthu chaching’ono kuti Mulungu anakuyandikizani kwa iye, limodzi ndi abale anu onse, ana a Levi? Kodi tsopano anthu inu mukufunanso udindo waunsembe?+