Numeri 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Mose anauza Kora+ kuti: “Mawa, iweyo ndi khamu lako lonse mukaonekere pamaso pa Yehova.+ Mukaonekere, iweyo limodzi ndi khamulo, ndi Aroni. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:16 Nsanja ya Olonda,8/1/2002, ptsa. 11-128/1/2000, tsa. 11
16 Kenako Mose anauza Kora+ kuti: “Mawa, iweyo ndi khamu lako lonse mukaonekere pamaso pa Yehova.+ Mukaonekere, iweyo limodzi ndi khamulo, ndi Aroni.