-
Numeri 16:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho aliyense wa iwo anatenga chofukizira chake n’kuikamo moto ndi nsembe yofukiza. Atatero, anakaimirira pakhomo la chihema chokumanako limodzi ndi Mose ndi Aroni.
-