Numeri 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Chotero iwo analowa m’nthaka, limodzi ndi onse amene anali kumbali yawo. Iwo anatsikira ku Manda ali amoyo. Nthakayo inawafotsera,+ moti iwo anafafanizika pakati pa mpingo wonse.+
33 Chotero iwo analowa m’nthaka, limodzi ndi onse amene anali kumbali yawo. Iwo anatsikira ku Manda ali amoyo. Nthakayo inawafotsera,+ moti iwo anafafanizika pakati pa mpingo wonse.+