Numeri 16:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Amuna inu, chokani pakati pa khamuli kuti ndilifafanize kamodzi n’kamodzi.”+ Atamva zimenezi, iwo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+
45 “Amuna inu, chokani pakati pa khamuli kuti ndilifafanize kamodzi n’kamodzi.”+ Atamva zimenezi, iwo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+