Numeri 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimene chichitike n’chakuti, munthu amene ndimusankheyo,+ ndodo yake idzaphuka, ndipo ndidzathetseratu kudandaula+ kwa ana a Isiraeli kumene akuchita motsutsana ndi ine, pamene akudandaula motsutsana nawe.”+
5 Chimene chichitike n’chakuti, munthu amene ndimusankheyo,+ ndodo yake idzaphuka, ndipo ndidzathetseratu kudandaula+ kwa ana a Isiraeli kumene akuchita motsutsana ndi ine, pamene akudandaula motsutsana nawe.”+