Numeri 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho, Mose analankhula ndi ana a Isiraeli. Aliyense wa atsogoleri awo anapereka ndodo+ yake, malinga ndi fuko lawo. Zinalipo ndodo 12, ndipo imodzi ya ndodozo+ inali ya Aroni.
6 Choncho, Mose analankhula ndi ana a Isiraeli. Aliyense wa atsogoleri awo anapereka ndodo+ yake, malinga ndi fuko lawo. Zinalipo ndodo 12, ndipo imodzi ya ndodozo+ inali ya Aroni.